Mateyu 15:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Pamenepo Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo kuchokera mu ola limenelo mwana wake anachira.+ Luka 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Yesu atamva zimenezi anadabwa ndi munthu ameneyu. Kenako anacheukira khamu la anthu omutsatira aja n’kunena kuti: “Kunena zoona, ngakhale mu Isiraeli sindinapezemo chikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.”+
28 Pamenepo Yesu anamuyankha kuti: “Mayi iwe, chikhulupiriro chako ndi chachikulu. Zimene ukufuna zichitike kwa iwe.” Ndipo kuchokera mu ola limenelo mwana wake anachira.+
9 Yesu atamva zimenezi anadabwa ndi munthu ameneyu. Kenako anacheukira khamu la anthu omutsatira aja n’kunena kuti: “Kunena zoona, ngakhale mu Isiraeli sindinapezemo chikhulupiriro chachikulu ngati chimenechi.”+