Mateyu 16:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+ Maliko 8:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine ndi uthenga wabwino, adzaupulumutsa.+ Luka 17:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Aliyense wofunitsitsa kusunga moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake adzausunga.+ Yohane 12:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+
25 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya, koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine adzaupeza.+
35 Pakuti aliyense wofuna kupulumutsa moyo wake adzautaya. Koma aliyense wotaya moyo wake chifukwa cha ine ndi uthenga wabwino, adzaupulumutsa.+
25 Aliyense wokonda moyo wake akuuwononga, koma wodana ndi moyo wake+ m’dziko lino akuusungira moyo wosatha.+