Luka 16:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Anthu anali kulalikira Chilamulo ndi Zolemba za aneneri kudzafika m’nthawi ya Yohane.+ Kuchokera nthawi imeneyo, uthenga wabwino umene ukulengezedwa ndi wokhudza ufumu wa Mulungu, ndipo anthu osiyanasiyana akuyesetsa mwakhama kuti akalowemo.+
16 “Anthu anali kulalikira Chilamulo ndi Zolemba za aneneri kudzafika m’nthawi ya Yohane.+ Kuchokera nthawi imeneyo, uthenga wabwino umene ukulengezedwa ndi wokhudza ufumu wa Mulungu, ndipo anthu osiyanasiyana akuyesetsa mwakhama kuti akalowemo.+