Mateyu 11:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti zonse, Zolemba za aneneri ndi Chilamulo, zinalosera mpaka nthawi ya Yohane.+