Maliko 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Afarisi anapita kwa iye n’kumufunsa kuti: “Taonani! N’chifukwa chiyani akuchita zosaloleka pa sabata?”+ Luka 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afarisi ena ataona zimenezi anati: “N’chifukwa chiyani mukuchita zosemphana ndi malamulo+ pa sabata?”+
24 Pamenepo Afarisi anapita kwa iye n’kumufunsa kuti: “Taonani! N’chifukwa chiyani akuchita zosaloleka pa sabata?”+
2 Afarisi ena ataona zimenezi anati: “N’chifukwa chiyani mukuchita zosemphana ndi malamulo+ pa sabata?”+