Mateyu 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Afarisi ataona zimenezi anamuuza kuti:+ “Taona! Ophunzira ako akuchita zosayenera kuzichita pa sabata.”+ Maliko 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pamenepo Afarisi anapita kwa iye n’kumufunsa kuti: “Taonani! N’chifukwa chiyani akuchita zosaloleka pa sabata?”+ Yohane 5:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Choncho Ayuda anayamba kuuza munthu wochiritsidwa uja kuti: “Lero ndi Sabata, n’kosaloleka+ kuti unyamule machirawa.”
2 Afarisi ataona zimenezi anamuuza kuti:+ “Taona! Ophunzira ako akuchita zosayenera kuzichita pa sabata.”+
24 Pamenepo Afarisi anapita kwa iye n’kumufunsa kuti: “Taonani! N’chifukwa chiyani akuchita zosaloleka pa sabata?”+
10 Choncho Ayuda anayamba kuuza munthu wochiritsidwa uja kuti: “Lero ndi Sabata, n’kosaloleka+ kuti unyamule machirawa.”