Maliko 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete. Luka 14:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamuona, Yesu analankhula ndi odziwa Chilamulo ndi Afarisiwo kuti: “Kodi n’kololeka kuchiritsa pa sabata kapena ayi?”+ Yohane 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.
4 Kenako anawafunsa kuti: “Kodi malamulo amalola kuchita chiti pa sabata? Chabwino kapena choipa? Kupulumutsa moyo kapena kupha?”+ Koma iwo anangokhala chete.
3 Atamuona, Yesu analankhula ndi odziwa Chilamulo ndi Afarisiwo kuti: “Kodi n’kololeka kuchiritsa pa sabata kapena ayi?”+
16 Ena mwa Afarisiwo anayamba kunena kuti: “Munthu ameneyu si wochokera kwa Mulungu, chifukwa sasunga Sabata.”+ Ena anayamba kunena kuti: “Koma munthu wochimwa angachite bwanji zizindikiro+ zoterezi?” Choncho panakhala kugawanika+ pakati pawo.