Genesis 49:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+ Mateyu 27:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+
10 Ndodo yachifumu sidzachoka kwa Yuda,+ ndiponso chibonga cha wolamulira sichidzachoka pakati pa mapazi ake, kufikira Silo*+ atabwera. Ndipo mitundu ya anthu idzamumvera.+
37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+