Maliko 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno mawu osonyeza mlandu wake+ anawalemba pamwamba pake kuti: “Mfumu ya Ayuda.”+ Luka 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamwamba pake analembapo mawu akuti: “Uyu ndiye mfumu ya Ayuda.”+ Yohane 19:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pilato analembanso dzina laudindo ndi kuliika pamtengo wozunzikirapowo. Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+
19 Pilato analembanso dzina laudindo ndi kuliika pamtengo wozunzikirapowo. Analemba kuti: “Yesu Mnazareti, Mfumu ya Ayuda.”+