Mateyu 27:37 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+ Maliko 15:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndiyeno mawu osonyeza mlandu wake+ anawalemba pamwamba pake kuti: “Mfumu ya Ayuda.”+ Luka 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Pamwamba pake analembapo mawu akuti: “Uyu ndiye mfumu ya Ayuda.”+
37 Komanso pamwamba pa mutu wake anakhomapo chikwangwani cha mawu osonyeza mlandu wake kuti: “Uyu ndi Yesu, Mfumu ya Ayuda.”+