Luka 11:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Nthawi inayake anali kutulutsa chiwanda cholepheretsa munthu kulankhula.+ Chiwandacho chitatuluka, munthu wosalankhulayo analankhula, ndipo khamu la anthu linadabwa kwambiri.
14 Nthawi inayake anali kutulutsa chiwanda cholepheretsa munthu kulankhula.+ Chiwandacho chitatuluka, munthu wosalankhulayo analankhula, ndipo khamu la anthu linadabwa kwambiri.