Maliko 4:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndithudi, sanalankhule nawo chilichonse popanda fanizo, koma kumbali anali kufotokoza zonse kwa ophunzira ake.+
34 Ndithudi, sanalankhule nawo chilichonse popanda fanizo, koma kumbali anali kufotokoza zonse kwa ophunzira ake.+