11 Koma iye anawayankha kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira zinsinsi zopatulika+ za ufumu wakumwamba, koma anthu amenewa sanapatsidwe mwayi umenewo.+
35 kuti zikwaniritsidwe zimene zinanenedwa kudzera mwa mneneri amene anati: “Ndidzatsegula pakamwa panga ndi kunena mafanizo, ndidzafalitsa zinthu zobisika kuchokera pa chiyambi cha dziko lapansi.”+
11 Ndipo iye anayamba kuwauza kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira chinsinsi chopatulika+ cha ufumu wa Mulungu. Koma kwa amene ali kunja zonse zimachitika mwa mafanizo,+