Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Koma iye anawayankha kuti: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira zinsinsi zopatulika+ za ufumu wakumwamba, koma anthu amenewa sanapatsidwe mwayi umenewo.+

  • Luka 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Iye anati: “Inu mwapatsidwa mwayi wozindikira zinsinsi zopatulika za ufumu wa Mulungu. Koma kwa enawo, zonse ndi mafanizo okhaokha.+ Izi zili choncho kuti kuona aziona ndithu, koma kukhale kopanda phindu, kumvanso azimva ndithu, koma asazindikire tanthauzo lake.+

  • Akolose 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pitirizani kuyenda mwanzeru pochita zinthu ndi anthu akunja,*+ ndipo muzigwiritsa ntchito bwino nthawi yanu.*+

  • 1 Timoteyo 3:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Komanso, akhale woti ngakhale anthu akunja* akumuchitira umboni wabwino,+ kuti asatonzedwe ndi kukodwa mumsampha+ wa Mdyerekezi.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena