Mateyu 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma atamva kuti Arikelao ndi amene akulamulira monga mfumu ya Yudeya m’malo mwa bambo ake Herode, anachita mantha kupita kumeneko. Komanso, chifukwa chakuti analandira chenjezo la Mulungu m’maloto,+ iwo anapita m’dera la Galileya.+
22 Koma atamva kuti Arikelao ndi amene akulamulira monga mfumu ya Yudeya m’malo mwa bambo ake Herode, anachita mantha kupita kumeneko. Komanso, chifukwa chakuti analandira chenjezo la Mulungu m’maloto,+ iwo anapita m’dera la Galileya.+