Maliko 1:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’masiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+ Luka 2:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Choncho, atachita zonse mogwirizana ndi chilamulo+ cha Yehova, anabwerera ku Galileya, kumzinda wawo wa Nazareti.+
9 M’masiku amenewo, Yesu anabwera kuchokera ku Nazareti wa ku Galileya ndipo anabatizidwa ndi Yohane mu Yorodano.+
39 Choncho, atachita zonse mogwirizana ndi chilamulo+ cha Yehova, anabwerera ku Galileya, kumzinda wawo wa Nazareti.+