Maliko 6:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ngakhale kuti mfumu inamva chisoni kwambiri, sinafune kumukanira poganizira lumbiro lake lija, komanso poganizira amene anali kudya nawo chakudya patebulopo.+
26 Ngakhale kuti mfumu inamva chisoni kwambiri, sinafune kumukanira poganizira lumbiro lake lija, komanso poganizira amene anali kudya nawo chakudya patebulopo.+