Maliko 6:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ophunzira ake atamva zimenezo anabwera kudzatenga mtembo wake ndi kukauika m’manda achikumbutso.+ Machitidwe 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amuna ena oopa Mulungu anatenga Sitefano ndi kukamuika m’manda,+ ndipo anamulira kwambiri.+