Mateyu 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pambuyo pake, ophunzira ake anabwera kudzatenga mtembo wake ndi kukauika m’manda.+ Kenako anapita kukauza Yesu. Machitidwe 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Koma amuna ena oopa Mulungu anatenga Sitefano ndi kukamuika m’manda,+ ndipo anamulira kwambiri.+
12 Pambuyo pake, ophunzira ake anabwera kudzatenga mtembo wake ndi kukauika m’manda.+ Kenako anapita kukauza Yesu.