Maliko 6:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 Iye anawauza kuti: “Inuyo bwerani kuno, tipite kwatokha kopanda anthu+ kuti mupumule pang’ono.”+ Pakuti ambiri anali kubwera ndi kupita, ndipo analibe nthawi yopuma, ngakhale yoti adye chakudya.+ Luka 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene iwo anachita.+ Atatero anawatenga ndi kupita nawo kwaokhaokha+ mumzinda wotchedwa Betsaida.
31 Iye anawauza kuti: “Inuyo bwerani kuno, tipite kwatokha kopanda anthu+ kuti mupumule pang’ono.”+ Pakuti ambiri anali kubwera ndi kupita, ndipo analibe nthawi yopuma, ngakhale yoti adye chakudya.+
10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene iwo anachita.+ Atatero anawatenga ndi kupita nawo kwaokhaokha+ mumzinda wotchedwa Betsaida.