Luka 9:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene anachita.+ Atatero anawatenga nʼkupita nawo kwaokha mumzinda wotchedwa Betsaida.+ Luka Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 9:10 Yesu—Ndi Njira, tsa. 128 Buku la Onse, tsa. 17 Nsanja ya Olonda,9/1/1987, tsa. 16
10 Atumwi aja atabwerako anafotokozera Yesu zimene anachita.+ Atatero anawatenga nʼkupita nawo kwaokha mumzinda wotchedwa Betsaida.+