Luka 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Komano nthawi inali itapita. Choncho atumwi 12 aja anafika ndi kumuuza kuti: “Auzeni anthuwa kuti anyamuke, apite m’midzi ndi m’madera apafupi kuti akapeze malo ogona ndi chakudya, chifukwa kumene tili kuno n’kopanda anthu.”+
12 Komano nthawi inali itapita. Choncho atumwi 12 aja anafika ndi kumuuza kuti: “Auzeni anthuwa kuti anyamuke, apite m’midzi ndi m’madera apafupi kuti akapeze malo ogona ndi chakudya, chifukwa kumene tili kuno n’kopanda anthu.”+