Salimo 78:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Pamenepo anayamba kulankhula mawu oipa kwa Mulungu.+Iwo anati: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya m’chipululu muno?”+ Mateyu 14:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma chakumadzulo ophunzira ake anabwera kwa iye ndi kunena kuti: “Kuno n’kopanda anthu ndipo nthawi yatha, auzeni anthuwa kuti anyamuke, apite m’midzimo kuti akagule chakudya.”+ Maliko 6:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Tsopano kunja kunada, ndipo ophunzira ake anabwera kwa iye ndi kunena kuti: “Kuno n’kopanda anthu, ndipo nthawi yatha.+ Yohane 6:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yesu atakweza maso ake ndi kuona khamu lalikulu la anthu likubwera kwa iye, anafunsa Filipo kuti: “Kodi mitanda ya mkate yodyetsa anthu onsewa tikaigula kuti?”+
19 Pamenepo anayamba kulankhula mawu oipa kwa Mulungu.+Iwo anati: “Kodi Mulungu angathe kutipatsa chakudya m’chipululu muno?”+
15 Koma chakumadzulo ophunzira ake anabwera kwa iye ndi kunena kuti: “Kuno n’kopanda anthu ndipo nthawi yatha, auzeni anthuwa kuti anyamuke, apite m’midzimo kuti akagule chakudya.”+
35 Tsopano kunja kunada, ndipo ophunzira ake anabwera kwa iye ndi kunena kuti: “Kuno n’kopanda anthu, ndipo nthawi yatha.+
5 Ndiyeno Yesu atakweza maso ake ndi kuona khamu lalikulu la anthu likubwera kwa iye, anafunsa Filipo kuti: “Kodi mitanda ya mkate yodyetsa anthu onsewa tikaigula kuti?”+