Maliko 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ndipo onse amene anadya mkatewo anali amuna okwana 5,000.+ Luka 9:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo panali amuna pafupifupi 5,000.+ Koma Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Auzeni akhale m’magulu, muja amakhalira akamadya chakudya. Pagulu lililonse pakhale anthu pafupifupi 50.”+ Yohane 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Yesu ananena kuti: “Akhazikeni pansi anthuwa muja amakhalira pa chakudya.”+ Pamalopo panali udzu wambiri. Choncho amuna pafupifupi 5,000 anakhaladi pansi.+
14 Pamenepo panali amuna pafupifupi 5,000.+ Koma Yesu anauza ophunzira ake kuti: “Auzeni akhale m’magulu, muja amakhalira akamadya chakudya. Pagulu lililonse pakhale anthu pafupifupi 50.”+
10 Yesu ananena kuti: “Akhazikeni pansi anthuwa muja amakhalira pa chakudya.”+ Pamalopo panali udzu wambiri. Choncho amuna pafupifupi 5,000 anakhaladi pansi.+