Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Mateyu 14:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kenako analamula khamu la anthulo kuti likhale pansi pa udzu. Pamenepo anatenga mitanda ya mkate isanu ija ndi nsomba ziwiri zija, n’kuyang’ana kumwamba ndi kupempha dalitso.+ Atatero ananyemanyema mitanda ya mkate ija n’kupatsa ophunzirawo, ndipo iwonso anagawira khamulo.+

  • Maliko 6:39
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 39 Kenako anauza anthuwo kuti akhale m’magulu+ pa udzu wobiriwira.+

  • 1 Akorinto 14:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Koma zinthu zonse zizichitika moyenera ndi mwadongosolo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena