Maliko 6:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo atatsazikana ndi anthuwo, iye anachoka n’kupita m’phiri kukapemphera.+ Luka 6:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 M’masiku amenewa, Yesu anapita kuphiri kukapemphera,+ ndipo anachezera kupemphera kwa Mulungu usiku wonse.+ Luka 9:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Nthawi inayake, pamene anali kupemphera payekha, ophunzira ake anafika kwa iye onse pamodzi. Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi anthuwa akumati ine ndine ndani?”+
12 M’masiku amenewa, Yesu anapita kuphiri kukapemphera,+ ndipo anachezera kupemphera kwa Mulungu usiku wonse.+
18 Nthawi inayake, pamene anali kupemphera payekha, ophunzira ake anafika kwa iye onse pamodzi. Ndiyeno iye anawafunsa kuti: “Kodi anthuwa akumati ine ndine ndani?”+