Maliko 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Iye anawayankha kuti: “Yesaya analosera moyenera za anthu onyenga inu, monga mmene Malemba amanenera kuti,+ ‘Anthu awa amandilemekeza ndi milomo yokha, koma mitima yawo ili kutali ndi ine.+
6 Iye anawayankha kuti: “Yesaya analosera moyenera za anthu onyenga inu, monga mmene Malemba amanenera kuti,+ ‘Anthu awa amandilemekeza ndi milomo yokha, koma mitima yawo ili kutali ndi ine.+