-
Mateyu 13:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Kenako atauza khamu la anthulo kuti lizipita, analowa m’nyumba. Ndipo ophunzira ake anabwera kwa iye ndi kunena kuti: “Timasulireni fanizo lija la namsongole m’munda.”
-