Maliko 7:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Atanyamuka kumeneko, analowera kumadera a Turo ndi Sidoni.+ Kumeneko anakalowa m’nyumba ina, ndipo sanafune kuti aliyense adziwe kuti ali kumeneko. Koma anthu anadziwabe.+
24 Atanyamuka kumeneko, analowera kumadera a Turo ndi Sidoni.+ Kumeneko anakalowa m’nyumba ina, ndipo sanafune kuti aliyense adziwe kuti ali kumeneko. Koma anthu anadziwabe.+