Maliko 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 M’masiku amenewo, khamu la anthu linasonkhananso, koma linalibe chakudya. Ndiyeno Yesu anaitana ophunzira ake ndi kuwauza kuti:+
8 M’masiku amenewo, khamu la anthu linasonkhananso, koma linalibe chakudya. Ndiyeno Yesu anaitana ophunzira ake ndi kuwauza kuti:+