Mateyu 15:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Koma Yesu anaitana ophunzira ake n’kunena kuti:+ “Khamu la anthuli likundimvetsa chisoni,+ chifukwa anthuwa akhala ndi ine masiku atatu tsopano ndipo alibe chakudya. Sindikufuna kuwauza kuti azipita asanadye, chifukwa angalenguke panjira.”
32 Koma Yesu anaitana ophunzira ake n’kunena kuti:+ “Khamu la anthuli likundimvetsa chisoni,+ chifukwa anthuwa akhala ndi ine masiku atatu tsopano ndipo alibe chakudya. Sindikufuna kuwauza kuti azipita asanadye, chifukwa angalenguke panjira.”