Maliko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yohane m’batizi anafika m’chipululu, ndipo anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Yohane 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Panaonekera munthu wina amene anatumidwa monga nthumwi ya Mulungu.+ Dzina lake anali Yohane.+
4 Yohane m’batizi anafika m’chipululu, ndipo anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+