Mateyu 3:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iye anali kulalikira kuti: “Lapani,+ pakuti ufumu wakumwamba wayandikira.”+ Luka 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anabwera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano. Anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Machitidwe 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa.
3 Choncho iye anabwera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano. Anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+
24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa.