Mateyu 3:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 M’masiku amenewo, Yohane M’batizi+ anapita m’chipululu+ cha Yudeya n’kuyamba kulalikira. Maliko 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yohane m’batizi anafika m’chipululu, ndipo anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+ Luka 1:77 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 77 Kukadziwitsa anthu ake za chipulumutso pokhululukidwa machimo awo,+ Machitidwe 13:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa.
4 Yohane m’batizi anafika m’chipululu, ndipo anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+
24 Mpulumutsi+ ameneyu asanafike, Yohane+ anali atalalikiriratu poyera kwa anthu onse mu Isiraeli za ubatizo, monga chizindikiro cha kulapa.