Luka 3:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iye anabwera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano. Anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+
3 Choncho iye anabwera m’midzi yonse yapafupi ndi Yorodano. Anali kulalikira za ubatizo monga chizindikiro cha kulapa kuti machimo akhululukidwe.+