Maliko 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malinga ndi zimenezo, patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane, n’kukwera nawo m’phiri lalitali, kwaokhaokha. Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo,+ Luka 9:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Patapita masiku pafupifupi 8 chinenereni mawu amenewa, iye anatenga Petulo, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera nawo m’phiri kukapemphera.+ 2 Petulo 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Zoonadi, mawu amenewa tinawamva+ kuchokera kumwamba tili naye limodzi m’phiri loyera.+
2 Malinga ndi zimenezo, patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane, n’kukwera nawo m’phiri lalitali, kwaokhaokha. Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo,+
28 Patapita masiku pafupifupi 8 chinenereni mawu amenewa, iye anatenga Petulo, Yohane ndi Yakobo ndi kukwera nawo m’phiri kukapemphera.+