Mateyu 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Patapita masiku 6 Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane m’bale wake, n’kukwera nawo m’phiri lalitali kwaokhaokha.+ Maliko 9:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malinga ndi zimenezo, patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane, n’kukwera nawo m’phiri lalitali, kwaokhaokha. Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo,+
17 Patapita masiku 6 Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane m’bale wake, n’kukwera nawo m’phiri lalitali kwaokhaokha.+
2 Malinga ndi zimenezo, patapita masiku 6, Yesu anatenga Petulo, Yakobo ndi Yohane, n’kukwera nawo m’phiri lalitali, kwaokhaokha. Kumeneko iye anasandulika pamaso pawo,+