Mateyu 16:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ine ndidzakupatsa makiyi a ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kumwamba.”+ Yohane 20:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Mukakhululukira munthu amene wachita tchimo,+ ndiye kuti Mulungu wamukhululukira kale. Koma mukapanda kukhululukira munthu amene wachita tchimo, ndiye kuti Mulungu sanamukhululukire.”+
19 Ine ndidzakupatsa makiyi a ufumu wakumwamba. Chilichonse chimene udzamanga padziko lapansi chidzakhala chitamangidwa kumwamba, ndipo chilichonse chimene udzamasula padziko lapansi chidzakhala chitamasulidwa kumwamba.”+
23 Mukakhululukira munthu amene wachita tchimo,+ ndiye kuti Mulungu wamukhululukira kale. Koma mukapanda kukhululukira munthu amene wachita tchimo, ndiye kuti Mulungu sanamukhululukire.”+