Luka 7:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 “Amuna awiri anatenga ngongole kwa munthu wina wokongoza ndalama. Mmodzi anatenga ngongole ya madinari 500,+ koma winayo anatenga ngongole ya madinari 50.
41 “Amuna awiri anatenga ngongole kwa munthu wina wokongoza ndalama. Mmodzi anatenga ngongole ya madinari 500,+ koma winayo anatenga ngongole ya madinari 50.