1 Akorinto 7:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ndikunena kwa osakwatira+ ndi kwa akazi amasiye kuti, ndi bwino akhalebe mmene ineyo ndililimu.+ 1 Akorinto 7:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Nayenso amene walekana ndi moyo wokhala yekha* n’kulowa m’banja wachita bwino,+ koma amene sanalowe m’banja wachita bwino koposa.+ 1 Akorinto 7:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Komabe angakhale wosangalala kwambiri ngati apitiriza mmene alili.+ Ndi mmene ine ndikuonera. Ndipo ndine wotsimikiza mtima kuti ndilinso ndi mzimu wa Mulungu.+
8 Tsopano ndikunena kwa osakwatira+ ndi kwa akazi amasiye kuti, ndi bwino akhalebe mmene ineyo ndililimu.+
38 Nayenso amene walekana ndi moyo wokhala yekha* n’kulowa m’banja wachita bwino,+ koma amene sanalowe m’banja wachita bwino koposa.+
40 Komabe angakhale wosangalala kwambiri ngati apitiriza mmene alili.+ Ndi mmene ine ndikuonera. Ndipo ndine wotsimikiza mtima kuti ndilinso ndi mzimu wa Mulungu.+