1 Akorinto 7:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Chotero ndikuganiza kuti zingakhale bwino, malinga ndi mavuto amene tili nawo, kuti mwamuna akhalebe mmene alili.+
26 Chotero ndikuganiza kuti zingakhale bwino, malinga ndi mavuto amene tili nawo, kuti mwamuna akhalebe mmene alili.+