1 Akorinto 7:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu aliyense akhale mmene Yehova wamugawira gawo lake,+ mmene Mulungu wamuitanira.+ Izi n’zimene ndikukhazikitsa+ m’mipingo yonse.
17 Munthu aliyense akhale mmene Yehova wamugawira gawo lake,+ mmene Mulungu wamuitanira.+ Izi n’zimene ndikukhazikitsa+ m’mipingo yonse.