1 Akorinto 7:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo.+ Komabe, aliyense ali ndi mphatso+ yake yochokera kwa Mulungu. Wina m’njira iyi, winanso m’njira inayo.
7 Koma ndikanakonda amuna onse akanakhala ngati ineyo.+ Komabe, aliyense ali ndi mphatso+ yake yochokera kwa Mulungu. Wina m’njira iyi, winanso m’njira inayo.