Deuteronomo 23:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 “Mwamuna wofulidwa+ mwa kuphwanya mavalo+ ake kapena woduka maliseche asalowe mumpingo wa Yehova. Yesaya 56:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mlendo yemwe wadziphatika kwa Yehova asanene kuti,+ ‘Ndithu Yehova adzandilekanitsa ndi anthu ake.’+ Nayenso munthu wofulidwa+ asanene kuti, ‘Ine ndiye ndine mtengo wouma basi.’”
3 Mlendo yemwe wadziphatika kwa Yehova asanene kuti,+ ‘Ndithu Yehova adzandilekanitsa ndi anthu ake.’+ Nayenso munthu wofulidwa+ asanene kuti, ‘Ine ndiye ndine mtengo wouma basi.’”