Yesaya 56:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu ofulidwa amene amasunga sabata langa, ndiponso amene asankha kuchita zimene ndimasangalala nazo,+ komanso amene amatsatira pangano langa,+ Mateyu 19:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pakuti ena sakwatira chifukwa chakuti anabadwa choncho kuchokera m’mimba mwa mayi awo,+ ndipo ena chifukwa chakuti anafulidwa ndi anthu. Koma pali ena amene safuna kukwatira chifukwa cha ufumu wakumwamba. Amene angathe kuchita zimenezi achite.”+
4 Pakuti Yehova wanena kuti: “Anthu ofulidwa amene amasunga sabata langa, ndiponso amene asankha kuchita zimene ndimasangalala nazo,+ komanso amene amatsatira pangano langa,+
12 Pakuti ena sakwatira chifukwa chakuti anabadwa choncho kuchokera m’mimba mwa mayi awo,+ ndipo ena chifukwa chakuti anafulidwa ndi anthu. Koma pali ena amene safuna kukwatira chifukwa cha ufumu wakumwamba. Amene angathe kuchita zimenezi achite.”+