Maliko 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano anthu anayamba kum’bweretsera ana aang’ono kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo anawakalipira.+ Luka 18:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Pamenepo anthu anayamba kumubweretsera ana kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo ataona zimenezo anayamba kuwakalipira.+
13 Tsopano anthu anayamba kum’bweretsera ana aang’ono kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo anawakalipira.+
15 Pamenepo anthu anayamba kumubweretsera ana kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo ataona zimenezo anayamba kuwakalipira.+