Mateyu 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kenako anthu anam’bweretsera ana aang’ono kuti awaike manja ndi kuwapempherera, koma ophunzirawo anawakalipira.+ Maliko 10:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Tsopano anthu anayamba kum’bweretsera ana aang’ono kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo anawakalipira.+
13 Kenako anthu anam’bweretsera ana aang’ono kuti awaike manja ndi kuwapempherera, koma ophunzirawo anawakalipira.+
13 Tsopano anthu anayamba kum’bweretsera ana aang’ono kuti awakhudze ndi manja ake, koma ophunzirawo anawakalipira.+