Maliko 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi itafika cha m’ma 12 koloko masana,* kunagwa mdima m’dziko lonselo mpaka 3 koloko masana.*+ Yohane 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipotu kumeneko kunali kasupe+ wa Yakobo. Yesu atatopa ndi ulendowo, anakhala pansi pakasupepo. Nthawi n’kuti ili cha m’ma 12 koloko masana.*
6 Ndipotu kumeneko kunali kasupe+ wa Yakobo. Yesu atatopa ndi ulendowo, anakhala pansi pakasupepo. Nthawi n’kuti ili cha m’ma 12 koloko masana.*