Mateyu 27:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kuyambira cha m’ma 12 koloko masana* kunagwa mdima+ m’dziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+ Luka 23:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Tsopano nthawi inali cha m’ma 12 koloko masana,* koma kunagwa mdima padziko lonse lapansi mpaka 3 koloko masana,*+
44 Tsopano nthawi inali cha m’ma 12 koloko masana,* koma kunagwa mdima padziko lonse lapansi mpaka 3 koloko masana,*+