Amosi 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limenelo ndidzachititsa kuti dzuwa lilowe masanasana,+ ndiponso kuti m’dziko mugwe mdima dzuwa lisanalowe. Mateyu 27:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Kuyambira cha m’ma 12 koloko masana* kunagwa mdima+ m’dziko lonselo, mpaka 3 koloko masana.*+ Maliko 15:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Nthawi itafika cha m’ma 12 koloko masana,* kunagwa mdima m’dziko lonselo mpaka 3 koloko masana.*+
9 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pa tsiku limenelo ndidzachititsa kuti dzuwa lilowe masanasana,+ ndiponso kuti m’dziko mugwe mdima dzuwa lisanalowe.